Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Uzimvera Yehova Mulungu wako mwa kuyenda m’njira zake,+ kusunga malamulo ake, zigamulo zake,+ ndi maumboni* ake, malinga ndi zimene zinalembedwa m’chilamulo cha Mose.+ Uzitero kuti udzakhale wanzeru m’zochita zako zonse, ndiponso kulikonse kumene udzapite.

  • Salimo 119:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Inu mwatilamula kuti tisunge+

      Malamulo anu mosamala.+

  • Ezekieli 44:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Inu simunakwaniritse utumiki wanu wosamalira zinthu zanga zopatulika,+ ndipo simunasankhe ena kuti azinditumikira pamalo anga opatulika m’malo mwa inu.”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena