Deuteronomo 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+ Deuteronomo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho muzisunga mawu a pangano ili kuti zonse zimene muzichita zizikuyenderani bwino.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
19 “Buku limeneli azikhala nalo nthawi zonse ndipo aziliwerenga masiku onse a moyo wake,+ kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wake ndi kusunga mawu onse a chilamulo ichi, kutinso azitsatira malangizo ake.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.