Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Yesaya 52:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Taona! Mtumiki wanga+ azidzachita zinthu mwanzeru.+ Iye adzakhala ndi udindo wapamwamba ndipo adzakwezedwa ndi kulemekezedwa kwambiri.+ Yesaya 53:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
13 Taona! Mtumiki wanga+ azidzachita zinthu mwanzeru.+ Iye adzakhala ndi udindo wapamwamba ndipo adzakwezedwa ndi kulemekezedwa kwambiri.+
11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+