Miyambo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali m’badwo umene umadziona kuti ndi woyera,+ koma sunasambe kuti uchotse ndowe zake.+ Ezekieli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Ndithu nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?’+
29 “‘Ndithu nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova n’zopanda chilungamo.”+ Kodi njira zanga ndiye zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira za anthu inu sindizo zopanda chilungamo?’+