Ekisodo 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+ Luka 1:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Kuchitira chifundo makolo athu akale ndi kukumbukira pangano lake loyera,+
24 M’kupita kwa nthawi, Mulungu anamva+ kubuula kwawo+ ndipo anakumbukira pangano lake ndi Abulahamu, Isaki ndi Yakobo.+