Maliko 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atadziyeretsa mwa kudziwaza madzi. Palinso miyambo ina yambiri+ imene anailandira ndipo akuisunga, monga kuviika makapu, mitsuko ndi ziwiya zamkuwa m’madzi+ . . .
4 Akabwera kuchokera kumsika, sadya mpaka atadziyeretsa mwa kudziwaza madzi. Palinso miyambo ina yambiri+ imene anailandira ndipo akuisunga, monga kuviika makapu, mitsuko ndi ziwiya zamkuwa m’madzi+ . . .