Mateyu 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, onyenga inu! Chifukwa mumayeretsa kunja kwa kapu+ ndi mbale, koma mkati mwake mutadzaza zolanda+ ndi kusadziletsa. Luka 11:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho Ambuye anamuuza kuti: “Inu Afarisi mumayeretsa kunja kwa kapu ndi mbale, koma mkati+ mwanu mwadzaza maganizo ofuna kulanda zinthu za anthu ndi kuchita zinthu zoipa.+
25 “Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, onyenga inu! Chifukwa mumayeretsa kunja kwa kapu+ ndi mbale, koma mkati mwake mutadzaza zolanda+ ndi kusadziletsa.
39 Choncho Ambuye anamuuza kuti: “Inu Afarisi mumayeretsa kunja kwa kapu ndi mbale, koma mkati+ mwanu mwadzaza maganizo ofuna kulanda zinthu za anthu ndi kuchita zinthu zoipa.+