Mateyu 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero pamene ukupereka mphatso zachifundo,+ usalize lipenga+ muja amachitira onyenga m’masunagoge ndi m’misewu, kuti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.
2 Chotero pamene ukupereka mphatso zachifundo,+ usalize lipenga+ muja amachitira onyenga m’masunagoge ndi m’misewu, kuti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, Amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.