Machitidwe 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ku Yopa+ kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene polimasulira limatanthauza Dorika.* Tabita anali kuchita ntchito zabwino zambiri,+ ndi kupereka mphatso zachifundo zochuluka. Machitidwe 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+ 1 Akorinto 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati ndapereka zanga zonse kudyetsa ena,+ ndipo ngati ndapereka thupi langa+ kuti ndidzitame, koma ndilibe chikondi,+ sindinapindule m’pang’ono pomwe.
36 Koma ku Yopa+ kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene polimasulira limatanthauza Dorika.* Tabita anali kuchita ntchito zabwino zambiri,+ ndi kupereka mphatso zachifundo zochuluka.
2 Iyeyu anali wopembedza+ ndi woopa+ Mulungu pamodzi ndi banja lake lonse. Anali kupatsa anthu mphatso zambiri zachifundo+ ndipo anali kupemphera kwa Mulungu nthawi zonse.+
3 Ngati ndapereka zanga zonse kudyetsa ena,+ ndipo ngati ndapereka thupi langa+ kuti ndidzitame, koma ndilibe chikondi,+ sindinapindule m’pang’ono pomwe.