Maliko 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsoka kwa akazi apakati ndi oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Luka 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa.
23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa.