Mateyu 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka kwa akazi apakati ndi oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Luka 19:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+ Luka 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa. Luka 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+
44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+
23 Tsoka kwa akazi apakati ndi kwa oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+ Pakuti m’dzikoli mudzakhala mavuto aakulu ndi mkwiyo pa anthu awa.
28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+