Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsoka kwa akazi apakati ndi oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+

  • Maliko 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsoka kwa akazi apakati ndi oyamwitsa ana m’masiku amenewo!+

  • Luka 19:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Iwo adzakuwononga+ limodzi ndi ana ako amene ali mwa iwe. Ndipo sadzasiya mwala pamwala unzake+ mwa iwe, chifukwa sunazindikire kuti nthawi yokuyendera inali itakwana.”+

  • Luka 23:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yesu anacheukira amayiwo ndi kunena kuti: “Ana aakazi a Yerusalemu inu, lekani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena