Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 17:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 M’masiku amenewo anthu anali kudya, kumwa, amuna anali kukwatira, akazi anali kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m’chingalawa, ndipo chigumula chinafika ndi kuwononga anthu onsewo.+

  • Aheberi 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mwa chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Mwa chikhulupiriro chimenecho, anatsutsa dziko,+ ndipo anakhala wolandira cholowa cha chilungamo,+ chimene chimabwera ndi chikhulupiriro.

  • 1 Petulo 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 imene inali yosamvera+ pa nthawi imene Mulungu anali kuleza mtima+ m’masiku a Nowa, pamene chingalawa chinali kupangidwa,+ chimene chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, miyoyo 8 yokha.+

  • 2 Petulo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anaperekanso chilango padziko lakale lija ndipo sanalilekerere,+ koma anasunga Nowa, mlaliki wa chilungamo,+ pomupulumutsa pamodzi ndi anthu ena 7,+ pamene anabweretsa chigumula+ padziko la anthu osaopa Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena