Mateyu 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Aliyense wakumva mawu angawa koma osawachita+ adzafanizidwa ndi munthu wopusa+ amene anamanga nyumba yake pamchenga.
26 Aliyense wakumva mawu angawa koma osawachita+ adzafanizidwa ndi munthu wopusa+ amene anamanga nyumba yake pamchenga.