Mateyu 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+
41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+