Deuteronomo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+ Maliko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo nthawi iliyonse imene mwafuna mungathe kuwachitira zabwino. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+
11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+
7 Pakuti osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo nthawi iliyonse imene mwafuna mungathe kuwachitira zabwino. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+