Maliko 14:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Nthawi yomweyo tambala analira kachiwiri.+ Pamenepo Petulo anakumbukira mawu amene Yesu anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire kawiri, udzandikana katatu.”+ Ndipo anamva chisoni ndi kuyamba kulira.+ Luka 22:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndipo anatuluka panja ndi kuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.+
72 Nthawi yomweyo tambala analira kachiwiri.+ Pamenepo Petulo anakumbukira mawu amene Yesu anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire kawiri, udzandikana katatu.”+ Ndipo anamva chisoni ndi kuyamba kulira.+