Luka 22:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Pamenepo Ambuye anacheuka ndi kuyang’ana Petulo, ndipo Petulo anakumbukira mawu amene Ambuye anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire lero, undikana katatu.”+ Yohane 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Petulo anakananso. Nthawi yomweyo tambala analira.+
61 Pamenepo Ambuye anacheuka ndi kuyang’ana Petulo, ndipo Petulo anakumbukira mawu amene Ambuye anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire lero, undikana katatu.”+