Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:74
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 74 Pamenepo iye anayamba kutemberera ndi kulumbira kuti: “Munthu ameneyu ine sindikumudziwa ayi!” Nthawi yomweyo tambala analira.+

  • Maliko 14:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Nthawi yomweyo tambala analira kachiwiri.+ Pamenepo Petulo anakumbukira mawu amene Yesu anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire kawiri, udzandikana katatu.”+ Ndipo anamva chisoni ndi kuyamba kulira.+

  • Luka 22:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo, mawu ali m’kamwa, tambala analira.+

  • Yohane 13:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Yesu anayankha kuti: “Kodi udzapereka moyo wako chifukwa cha ine? Ndithudi ndikukuuza iwe, Tambala asanalire undikana katatu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena