Luka 22:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo, mawu ali m’kamwa, tambala analira.+ Yohane 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Petulo anakananso. Nthawi yomweyo tambala analira.+
60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo, mawu ali m’kamwa, tambala analira.+