Mateyu 26:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Pamenepo iye anayamba kutemberera ndi kulumbira kuti: “Munthu ameneyu ine sindikumudziwa ayi!” Nthawi yomweyo tambala analira.+ Maliko 14:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Koma iye anayamba kudzitemberera ndi kulumbira kuti:+ “Munthu amene mukunenayu ine sindikumudziwa ayi.”+ Yohane 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Petulo anakananso. Nthawi yomweyo tambala analira.+
74 Pamenepo iye anayamba kutemberera ndi kulumbira kuti: “Munthu ameneyu ine sindikumudziwa ayi!” Nthawi yomweyo tambala analira.+
71 Koma iye anayamba kudzitemberera ndi kulumbira kuti:+ “Munthu amene mukunenayu ine sindikumudziwa ayi.”+