Mateyu 26:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Tsopano Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja, akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja n’kuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.+ Maliko 14:72 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Nthawi yomweyo tambala analira kachiwiri.+ Pamenepo Petulo anakumbukira mawu amene Yesu anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire kawiri, udzandikana katatu.”+ Ndipo anamva chisoni ndi kuyamba kulira.+
75 Tsopano Petulo anakumbukira mawu a Yesu aja, akuti: “Tambala asanalire, udzandikana katatu.”+ Ndipo anatuluka panja n’kuyamba kulira mopwetekedwa mtima kwambiri.+
72 Nthawi yomweyo tambala analira kachiwiri.+ Pamenepo Petulo anakumbukira mawu amene Yesu anamuuza aja, akuti: “Tambala asanalire kawiri, udzandikana katatu.”+ Ndipo anamva chisoni ndi kuyamba kulira.+