Luka 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Asilikali nawonso anamuchitira zachipongwe,+ anamuyandikira ndi kumupatsa vinyo wowawasa+ Yohane 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamalopo panali chiwiya chodzaza vinyo wowawasa. Pamenepo anatenga chinkhupule chimene anachiviika m’vinyo wowawasayo n’kuchisomeka kukamtengo ka hisope ndi kuchifikitsa pakamwa pake.+
29 Pamalopo panali chiwiya chodzaza vinyo wowawasa. Pamenepo anatenga chinkhupule chimene anachiviika m’vinyo wowawasayo n’kuchisomeka kukamtengo ka hisope ndi kuchifikitsa pakamwa pake.+