Salimo 69:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma anandipatsa chomera chakupha kuti ndidye,+Ndipo anayesa kundimwetsa vinyo wowawasa pamene ndinali ndi ludzu.+ Mateyu 27:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga chinkhupule ndi kuchiviika m’vinyo wowawasa+ ndipo anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe.+ Maliko 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma wina anathamanga kukaviika chinkhupule m’vinyo wowawasa, kenako anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe,+ ndikunena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”+ Luka 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Asilikali nawonso anamuchitira zachipongwe,+ anamuyandikira ndi kumupatsa vinyo wowawasa+
21 Koma anandipatsa chomera chakupha kuti ndidye,+Ndipo anayesa kundimwetsa vinyo wowawasa pamene ndinali ndi ludzu.+
48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga chinkhupule ndi kuchiviika m’vinyo wowawasa+ ndipo anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe.+
36 Koma wina anathamanga kukaviika chinkhupule m’vinyo wowawasa, kenako anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe,+ ndikunena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”+