Salimo 69:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma anandipatsa chomera chakupha kuti ndidye,+Ndipo anayesa kundimwetsa vinyo wowawasa pamene ndinali ndi ludzu.+ Mateyu 27:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga chinkhupule ndi kuchiviika m’vinyo wowawasa+ ndipo anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe.+ Yohane 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamalopo panali chiwiya chodzaza vinyo wowawasa. Pamenepo anatenga chinkhupule chimene anachiviika m’vinyo wowawasayo n’kuchisomeka kukamtengo ka hisope ndi kuchifikitsa pakamwa pake.+
21 Koma anandipatsa chomera chakupha kuti ndidye,+Ndipo anayesa kundimwetsa vinyo wowawasa pamene ndinali ndi ludzu.+
48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga chinkhupule ndi kuchiviika m’vinyo wowawasa+ ndipo anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe.+
29 Pamalopo panali chiwiya chodzaza vinyo wowawasa. Pamenepo anatenga chinkhupule chimene anachiviika m’vinyo wowawasayo n’kuchisomeka kukamtengo ka hisope ndi kuchifikitsa pakamwa pake.+