Maliko 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma wina anathamanga kukaviika chinkhupule m’vinyo wowawasa, kenako anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe,+ ndikunena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”+
36 Koma wina anathamanga kukaviika chinkhupule m’vinyo wowawasa, kenako anachiika kubango ndi kum’patsa kuti amwe,+ ndikunena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”+