Maliko 15:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 amene anali kuyenda naye limodzi+ ndi kumutumikira pamene anali ku Galileya. Panalinso amayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu.+ Luka 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.
41 amene anali kuyenda naye limodzi+ ndi kumutumikira pamene anali ku Galileya. Panalinso amayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu.+
3 Jowana+ mkazi wa Kuza kapitawo wa Herode, Suzana ndi amayi ena ambiri, amene anali kutumikira Yesu ndi atumwiwo pogwiritsa ntchito chuma chawo.