Maliko 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma Mariya Mmagadala ndi Mariya mayi wa Yose, anali kuyang’anitsitsa pamene anaikidwapo.+ Luka 23:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma amayi amene anayenda limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira kukaona manda achikumbutsowo+ ndi mmene mtembo wakewo anauikira.+
55 Koma amayi amene anayenda limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira kukaona manda achikumbutsowo+ ndi mmene mtembo wakewo anauikira.+