Mateyu 27:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Mariya Mmagadala ndi Mariya wina anatsalira komweko, atakhala pansi pafupi ndi mandawo.+ Luka 23:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma amayi amene anayenda limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira kukaona manda achikumbutsowo+ ndi mmene mtembo wakewo anauikira.+
55 Koma amayi amene anayenda limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira kukaona manda achikumbutsowo+ ndi mmene mtembo wakewo anauikira.+