Luka 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo anakweza maso ake ndi kuyang’ana ophunzira ake, ndipo anawauza kuti:+ “Odala ndinu osaukanu,+ chifukwa ufumu wa Mulungu ndi wanu. 1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
20 Pamenepo anakweza maso ake ndi kuyang’ana ophunzira ake, ndipo anawauza kuti:+ “Odala ndinu osaukanu,+ chifukwa ufumu wa Mulungu ndi wanu.
14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.