Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo. Maliko 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+ Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati m’bale wako wachita tchimo um’dzudzule,+ ndipo akalapa umukhululukire.+
25 Ndipo mukaimirira n’kumapemphera,+ khululukani chilichonse chimene wina anakulakwirani kuti Atate wanu wakumwamba akukhululukireni machimo anunso.”+