Ekisodo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite chigololo.+ Deuteronomo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Usachite chigololo.+ Luka 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe umadziwa malamulo+ akuti, ‘Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,*+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama+ ndiponso lakuti, Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+ Aroma 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa malamulo onena kuti, “Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,+ Usabe,+ Usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili m’mawu awa akuti, “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+
20 Iwe umadziwa malamulo+ akuti, ‘Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,*+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama+ ndiponso lakuti, Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+
9 Chifukwa malamulo onena kuti, “Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,+ Usabe,+ Usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili m’mawu awa akuti, “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+