Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+ Mateyu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anayankha kuti: “Chifukwa cha kuuma mtima kwanu,+ Mose anakulolezani kuti muzithetsa ukwati, koma kuyambira pa chiyambi sizinali choncho ayi.+ Maliko 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anati: “Mose analola kuti munthu akafuna kusiya mkazi wake azilemba kalata yothetsa ukwati ndi kum’siya mkaziyo.”+
24 “Mwamuna akatenga mkazi kuti akhale mkazi wake, ndiyeno ngati mkaziyo sanamusangalatse chifukwa wam’peza ndi vuto linalake,+ azimulembera kalata yothetsera ukwati+ ndi kum’patsa m’manja mwake, n’kumuchotsa panyumba pake.+
8 Iye anayankha kuti: “Chifukwa cha kuuma mtima kwanu,+ Mose anakulolezani kuti muzithetsa ukwati, koma kuyambira pa chiyambi sizinali choncho ayi.+
4 Iwo anati: “Mose analola kuti munthu akafuna kusiya mkazi wake azilemba kalata yothetsa ukwati ndi kum’siya mkaziyo.”+