Mateyu 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zimene zafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa m’nthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula, ndipo iye amakhala wosabala zipatso.+ Luka 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+
22 Zimene zafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa m’nthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula, ndipo iye amakhala wosabala zipatso.+
9 “Nanunso ndikukuuzani kuti, Dzipezereni mabwenzi+ ndi chuma chosalungama,+ kuti chumacho chikatha, akakulandireni m’malo okhala amuyaya.+