Luka 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Onetsetsani mmene maluwa amakulira.+ Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani, Ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati duwa lililonse mwa maluwa amenewa.+
27 Onetsetsani mmene maluwa amakulira.+ Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani, Ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati duwa lililonse mwa maluwa amenewa.+