Luka 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ganizirani za mmene maluwa amakulira: Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani kuti ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati lililonse la maluwa amenewa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 20-21
27 Ganizirani za mmene maluwa amakulira: Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani kuti ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati lililonse la maluwa amenewa.+