Luka 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Onetsetsani mmene maluwa amakulira.+ Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani, Ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati duwa lililonse mwa maluwa amenewa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:27 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 20-21
27 Onetsetsani mmene maluwa amakulira.+ Iwo sagwira ntchito kapena kuwomba nsalu. Koma ndikukuuzani, Ngakhale Solomo mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati duwa lililonse mwa maluwa amenewa.+