Maliko 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma pamene anali kudutsa, anaona Levi+ mwana wa Alifeyo, atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Pamenepo Levi ananyamuka ndi kumutsatira.+
14 Koma pamene anali kudutsa, anaona Levi+ mwana wa Alifeyo, atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.” Pamenepo Levi ananyamuka ndi kumutsatira.+