Mateyu 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina wotchedwa Mateyu atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Nthawi yomweyo ananyamuka ndi kum’tsatira.+
9 Atachoka pamenepo, Yesu anaona munthu wina wotchedwa Mateyu atakhala pansi mu ofesi yokhomera msonkho, ndipo anamuuza kuti: “Ukhale wotsatira wanga.”+ Nthawi yomweyo ananyamuka ndi kum’tsatira.+