Mateyu 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+ Luka 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Adzafika masiku pamene mudzalakalaka kuona limodzi la masiku a Mwana wa munthu koma simudzaliona.+
2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+
22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Adzafika masiku pamene mudzalakalaka kuona limodzi la masiku a Mwana wa munthu koma simudzaliona.+