Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Tsiku limeneli lidzakhala chikumbutso kwa inu, ndipo muzichitira Yehova chikondwerero m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale, kuti muzichita chikondwerero chimenechi.

  • Maliko 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti pasika+ ndi chikondwerero+ cha mikate yopanda chofufumitsa zichitike.+ Ndipo ansembe aakulu ndi alembi anali kufunafuna njira yogwirira Yesu mochenjera ndi kumupha.+

  • Luka 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa, chotchedwanso kuti Pasika,+ chinali kuyandikira.

  • Yohane 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano Yesu anadziwiratu chikondwerero cha pasika chisanafike, kuti nthawi yake yochoka m’dzikoli kupita kwa Atate+ yakwana.+ Ndipo popeza kuti anali kuwakonda akewo amene anali m’dzikoli,+ anawakonda mpaka pa mapeto a moyo wake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena