Luka 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti mzimu woyera+ udzakuphunzitsani mu ola lomwelo zoyenera kunena.”+ Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+