Maliko 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati ufumu wagawanika, ufumu umenewo sungakhale.+ Luka 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha, ndipo nyumba yogawanika imagwa.+
17 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha, ndipo nyumba yogawanika imagwa.+