Mateyu 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa. Maliko 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati ufumu wagawanika, ufumu umenewo sungakhale.+
25 Podziwa maganizo awo,+ iye anawauza kuti: “Ufumu uliwonse wogawanika umatha,+ ndipo mzinda uliwonse kapena nyumba yogawanika siikhalitsa.