Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kodi anthu amene atengedwa kale angalandidwe m’manja mwa munthu wamphamvu,+ kapena kodi gulu la anthu amene agwidwa ndi wolamulira wankhanza lingathawe?+

  • Maliko 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kunena zoona, palibe amene angalowe m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda+ katundu wake ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba. Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+

  • Luka 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma wina wamphamvu kuposa iyeyu+ akabwera n’kumugonjetsa,+ amamulanda zida zake zonse zimene amadalira, ndipo katundu amene wamulanda, amamugawa kwa ena.

  • 1 Yohane 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana okondedwa, inu ndinu ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa anthu amenewo,+ chifukwa amene muli ogwirizana+ naye ndi wamkulu+ kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena