Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kapena munthu angalowe bwanji m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda katundu wake, ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba? Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+

  • Maliko 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kunena zoona, palibe amene angalowe m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda+ katundu wake ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba. Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena