Maliko 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Wofesayo amafesa mawu.+ Luka 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma fanizoli+ tanthauzo lake ndi ili: Mbewuzo ndi mawu a Mulungu.+