Machitidwe 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma tsopano ndikukuperekani kwa Mulungu+ ndi ku mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni+ ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyeretsedwa onse.+ 1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+
32 Koma tsopano ndikukuperekani kwa Mulungu+ ndi ku mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu. Mawu amenewo angakulimbikitseni+ ndi kukupatsani cholowa pakati pa oyeretsedwa onse.+
23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+