Mateyu 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo ananena kuti: “Ili kuti mfumu ya Ayuda imene yabadwa?+ Chifukwa pamene tinali kum’mawa, tinaona nyenyezi+ yake ndipo tabwera kudzaigwadira.”
2 Iwo ananena kuti: “Ili kuti mfumu ya Ayuda imene yabadwa?+ Chifukwa pamene tinali kum’mawa, tinaona nyenyezi+ yake ndipo tabwera kudzaigwadira.”