Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano izi zinamveka kwa Mfumu Herode,* chifukwa dzina la Yesu linamveka paliponse. Anthu anali kunena kuti: “Yohane m’batizi wauka kwa akufa, ndipo pa chifukwa chimenechi akuchita ntchito zamphamvu.”+

  • Luka 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano Herode* wolamulira chigawo anamva zonse zimene zinali kuchitika. Iye anathedwa nzeru chifukwa ena anali kunena kuti Yohane anauka kwa akufa.+

  • Machitidwe 4:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode,* Pontiyo Pilato,+ pamodzi ndi anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzinda uno ndi kuukira Yesu, mtumiki wanu woyera,+ amene inu munamudzoza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena